Exodus 21:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Munthu akamenya kapolo wamwamuna kapena wamkazi pa diso, nkulikoloola disolo, ammasule kapoloyo, kuti akhale mfulu chifukwa cha disolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu akampanda mnyamata wake, kapena mdzakazi wake, padiso, nalithudzula, azimlola amuke waufulu chifukwa cha diso lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati munthu amenya wantchito wake wa mwamuna kapena mdzakazi wake pa diso ndi kuliwononga, wantchitoyo amasulidwe ngati malipiro a diso lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu akampanda mnyamata wace, kapena mdzakazi wace, padiso, nalithudzula, azimlola amuke waufulu cifukwa ca diso lace.