Exodus 21:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akamchotsa dzino, ammasule kapoloyo, kuti akhale mfulu chifukwa cha dzinolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akagulula dzino la mnyamata wake, kapena dzino la mdzakazi wake, azimlola amuke waufulu chifukwa cha dzino lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ngati agulula dzino la wantchito wamwamuna kapena mdzakazi, wantchitoyo amasulidwe ngati malipiro a dzino lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akagurula dzino la mnyamata wace, kapena dzino la mdzakazi wace, azimlola amuke waufulu cifukwa ca dzino lace.