Exodus 21:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati amlamula kuti adziwombole, adzayenera kulipira ndalama, kuti apulumutse moyo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akamuikira dipo, azipereka chiombolo cha moyo wake monga mwa zonse adamuikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati wauzidwa kuti alipire, iye apereke zimene wauzidwazo kuti awombole moyo wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akamuikira dipo, azipereka ciombolo ca moyo wace monga mwa zonse adamuikira.