Exodus 21:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ng'ombe ikapha mnyamata kapena mtsikana, lamulo lake ndi lomwelo ndithu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ingakhale yatunga mwana wamwamuna kapena wamkazi, aichitire monga mwa chiweruzo ichi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lamulo ili ligwirenso ntchito ngati ngʼombeyo yagunda mwana wamwamuna kapena wamkazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ingakhale yatunga mwana wamwamuna kapena wamkazi, aicitire monga mwa ciweruzo ici.