Exodus 21:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ayenera kulipira chifukwa cha choŵetacho. Alipire ndalama kwa mwini choŵetacho, koma nyamayo atenge ikhale yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mwini dzenje azilipa; azilipa ndalama kwa mwini nyamayo, koma yakufayo ndi yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mwini dzenjelo amulipire mwini chiweto chakufacho koma iye atenge chiwetocho.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mwini dzenje azilipa; azilipa ndalama kwa mwini nyamayo, koma yakufayo ndi yace.