Exodus 21:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kapoloyo akanena kuti, ‘Ndimakonda mbuyanga, mkazi wanga ndi ana anga, sindifuna kuti ndimasulidwe,’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mnyamatayo akanenetsa, Ndikonda mbuye wanga, mkazi wanga, ndi ana anga; sindituluka waufulu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma ngati kapoloyo alengeza kuti, ‘Ine sindikufuna kumasulidwa chifukwa ndimakonda mbuye wanga, mkazi wanga ndi ana,’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mnyamatayo akanenetsa, Ndikonda mbuye wanga, mkazi wanga, ndi ana anga; sindituruka waufulu;