Exodus 21:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Munthu akagulitsa mwana wake wamkazi ku ukapolo, mwanayo sadzaomboledwa monga m'mene amachitira ndi akapolo aamuna.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munthu akagulitsa mwana wake wamkazi akhale mdzakazi, iyeyu asatuluke monga amatuluka anyamata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati munthu agulitsa mwana wake wamkazi kukhala mdzakazi, mwanayo asamasulidwe monga achitira ndi akapolo aamuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo munthu akagulitsa mwana wace wamkazi akhale mdzakazi, iyeyo asaturuke monga amaturuka anyamata.