Exodus 21:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akaganiza zopatsa mwana wake mkaziyo, azidzamsunga ngati mwana wake wamkazi ndithu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati amtomera mwana wake wamwamuna, amchitire monga kuyenera ana akazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati anamusankha kuti akhale mkazi wa mwana wake, ayenera kumusunga ngati mwana wake wamkazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati amtomera mwana wace wamwamuna, amcitire monga kuyenera ana akazi.