Exodus 22:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati chidajiwa ndi zilombo, atengeko zotsalira zake kuti zikhale mboni, koma asalipire chimene chidajiwa ndi zilombocho.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati chajiwa ndithu, abwere nacho chikhale mboni; asalipe pa chojiwacho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati chinagwidwa ndi zirombo, iye ayenera kubweretsa zotsalira ngati umboni ndipo sadzalipira kanthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati cajiwa ndithu, abwere naco cikhale mboni; asalipe pa cojiwaco.