Exodus 22:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati bambo wake wa namwaliyo akana kuti mwana wakeyo asakwatiwe, munthuyo adzangolipirabe ndalama za chiwongo cha namwali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atate wake akakana konse kumpatsa iye, alipe ndalama monga mwa cholipa cha anamwali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati abambo ake akanitsitsa kwamtuwagalu kumupereka kuti amukwatire, munthuyo aperekebe malowolo woyenera namwaliyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atate wace akakana konse kumpatsa iye, alipe ndalama monga mwa colipa ca anamwali.