Exodus 22:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ngati mbala ipezeka ikuthyola nyumba ndipo ikanthidwa nkufa, asalipsire magazi chifukwa cha mbalayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akampeza wakuba alimkuboola, nakamkantha kotero kuti wafa, palibe chamwazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati mbala ipezeka ikuthyola nyumba ndipo imenyedwa nʼkufa, amene wapha mbalayo sanalakwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akampeza wakuba alimkuboola, nakamkantha kotero kuti wafa, palibe camwazi.