Exodus 23:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Usachite umboni wonama. Munthu wolakwa usamthandize pakumchitira umboni wonama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usatola mbiri yopanda pake; usathandizana naye woipa ndi kukhala mboni yochititsa chiwawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Usafalitse mbiri yabodza. Usathandize munthu wolakwa pomuchitira umboni wonama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usatola mbiri yopanda pace; usathandizana naye woipa ndi kukhala mboni yocititsa ciwawa.