Exodus 23:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzapirikitsa Ahivi, Akanani ndi Ahiti, inu musanafike, ndipo adzathaŵa monga ngati ndaŵatumira mavu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzatumiza mavu akutsogolere amene adzaingitsa Ahivi, Akanani, ndi Ahiti, pamaso pako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ahivi, Akanaani ndi Ahiti adzathawa ngati kuti ndawatumizira mavu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzatumiza mabvu akutsogolere amene adzaingitsa Ahivi, Akanani, ndi Ahiti, pamaso pako.