Exodus 23:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Asadzakhale m'dziko mwanu, kuwopa kuti angadzakuchimwitseni. Mukamapembedza milungu yao, ndithu mudzakodwa mu msampha.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asakhale m'dziko lako iwowa, kuti angakulakwitse pa Ine; pakuti ukatumikira milungu yao, kudzakukhalira msampha ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Asadzakhale mʼdziko lanu chifukwa angadzakuchimwitseni ndi kuyamba kupembedza milungu yawo. Mukadzatero ndiye kuti mwakodwa mu msampha.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asakhale m'dziko lako iwowa, kuti angakulakwitse pa loe; pakuti ukatumikira milungu yao, kudzakukhalira msampha ndithu.