Exodus 23:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ukaona ng'ombe ya mdani wako ikusokera, kapena bulu wake, utenge ukampatse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ukakomana ndi ng'ombe kapena bulu wa mdani wako zilimkusokera, uzimbwezera izo ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati ukumana ndi ngʼombe kapena bulu wa mdani wako zitasochera, uwonetsetse kuti wazitenga kupita nazo kwa mwini wakeyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukakomana ndi ng'ombe kapena buru wa mdani wako zirimkusokera, uzimbwezera izo ndithu.