Exodus 24:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose adatengako theka la magazi, naŵathira m'mbale, ndipo magazi otsala adawaza pa guwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anagawa mwaziwo, nathira wina m'zotengera, nawaza wina pa guwa la nsembe
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anatenga theka la magazi ndi kuyika mʼmbale, ndipo theka linalo analiwaza pa guwa lansembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose anagawa mwaziwo, nathira wina m'zotengera, nawaza wina pa guwa la nsembe.