Exodus 25:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndipo apange bokosi la matabwa a mtengo wa kasiya. Kutalika kwake kukhale masentimita 114, muufupi mwake masentimita 69, msinkhu wake masentimita 69.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo azipanga likasa la mtengo wakasiya: utali wake mikono iwiri ndi hafu, kupingasa kwake mkono ndi hafu, msinkhu wake mkono ndi hafu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsono apange bokosi lamatabwa amtengo wa mkesha, ndipo kutalika kwake kukhale masentimita 114, mulifupi mwake masentimita 69, msinkhu wake masentimita 69.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo azipanga likasa la mtengo wasitimu: utali wace mikono iwiri ndi hafu, kupingasa kwace mkono ndi hafu, msinkhu wace mkono ndi hafu.