Exodus 25:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Upange mphiko zonyamulira za mtengo wa kasiya, ndipo uzikute ndi golide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo uzipanga mphiko za mtengo wakasiya, ndi kuzikuta ndi golide, kuti anyamulire nazo gome.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Upange nsichi zamtengo wa mkesha ndi kuzikuta ndi golide kuti azinyamulira tebulolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo uzipanga mphiko za mtengo wasitimu, ndi kuzikuta ndi golidi, kuti anyamulire nazo gome.