Exodus 25:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
nsalu zobiriŵira, zofiirira ndi zofiira, nsalu zokoma zathonje, nsalu zopangidwa ndi ubweya wambuzi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, ndi ubweya wa mbuzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nsalu zobiriwira, zapepo, zofiira, nsalu zofewa, ubweya wambuzi;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi lamadzi, ndi: lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, ndi ubweya wa mbuzi;