Exodus 25:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mafuta a nyale, zonunkhira za mafuta odzozera, ndiponso lubani wa fungo lokoma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mafuta akuunikira, zonunkhira za mafuta odzoza, ndi za chofukiza cha fungo lokoma;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mafuta anyale a olivi, zonunkhiritsa mafuta odzozera ndi zopangira lubani wonunkhira;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mafuta akuunikira, zonunkhira za mafuta odzoza, ndi za cofukiza ca pfungo lokoma;