Exodus 25:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ulandirenso miyala yokoma ya onikisi, ndiponso miyala ina yoti uike pa chovala chaunsembe cha efodi, ndi pa chovala chapachifuwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
miyala yaberulo, ndi miyala yoika paefodi, ndi pachapachifuwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
miyala yokongola ya mtundu wa onikisi ndi ina yabwino yoyika pa efodi ndi pa chovala cha pachifuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
miyala yaberulo, ndi miyala yoika paefodi, ndi pacapacifuwa.