Exodus 26:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Popanga mafulemuwo, ku mbali yakumwera, upange makumi aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo uzipanga matabwa a Kachisi, matabwa makumi awiri ku mbali ya kumwera, kumwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Upange maferemu makumi awiri a mbali yakummwera kwa chihemacho.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo uzipanga matabwa a kacisi, matabwa makumi awiri ku mbali ya kumwela, kumwela.