Exodus 26:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo kumpoto kwa chihemacho upangenso mafulemu makumi aŵiri,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi pa mbali yake ina ya Kachisi, mbali ya kumpoto, pakhale matabwa makumi awiri; ndi makamwa asiliva makumi anai;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mbali yakumpoto ya chihemacho upangenso maferemu makumi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi pa mbali yace yina ya kacisi, mbali ya kumpoto, pakhale matabwa makumi awiri; ndi makamwa asiliva makumi anai;