Exodus 26:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndi masinde makumi anai asiliva, aŵiri pa fulemu lililonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Upangenso matsinde 40 asiliva, awiri pansi pa feremu iliyonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina.