Exodus 26:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumbuyo kwa chihema konko, pangodya pakhale mafulemu aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nupange matabwa awiri angodya za Kachisi za kumbuyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo upangenso maferemu awiri a pa ngodya yakumbuyo kwenikweni kwa tenti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nupange matabwa awiri a ngondya za kacisi za kumbuyo.