Exodus 26:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndi isanu inanso pa mafulemu a mbali ina. Pakhalenso mitanda isanu pa mafulemu akuzambwe chakumbuyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ina ya Kachisi, ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ya Kachisi ya kumbuyo kumadzulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mitanda isanu inanso ikhale ya maferemu a mbali inayo. Pakhalenso mitanda ina isanu ya mbali yakumadzulo, kumapeto kwenikweni kwa chihema.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi mitanda isanu ya matabwa a Pel mbali yina ya kacisi, ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ya kacisi ya kumbuyo kumadzulo.