Exodus 26:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtanda wa pakati penipeni pa mafulemuwo ugwire mafulemu onse, kuyambira ku mapeto mpaka ku mapeto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi mtanda wa pakati pa matabwa ufikire kuthungo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtanda wapakati pa maferemuwo uchokere pa maferemu a mbali ina mpaka mbali inanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mtanda wa pakati pa matabwa ufikire kuthungo.