Exodus 26:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Upange timagonga ta nsalu yobiriŵira m'mbali mwake mwa nsalu imodzi kumapeto kwake. Uchitenso chimodzimodzi ndi nsalu inzakeyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo uziika magango a nsalu ya madzi m'mphepete mwake mwa nsalu imodzi, ku mkawo wa chilumikizano; nuchite momwemo m'mphepete mwake mwa nsalu ya kuthungo ya chilumikizano china.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Panga zokolowekamo za nsalu yobiriwira mʼmphepete mwa nsalu imodzi yotsiriza ya mbali ina. Uchitenso chimodzimodzi ndi nsalu yotsiriza ya mbali inayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo uziika magango a nsaru yamadzi m'mphepete mwace mwa nsaru imodzi, ku mkawo wa cilumikizano; nucite momwemo m'mphepete mwace mwa nsaru ya kuthungoya cilumikizano dna.