Exodus 28:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Miyala imeneyi ikhalepo khumi ndi iŵiri, potsata maina a mafuko a Aisraele. Miyalayo izokotedwe ngati zidindo, uliwonse ukhale ndi dzina la fuko limodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi miyalayi ikhale monga mwa maina a ana a Israele, khumi ndi awiri, monga maina ao; monga malochedwe a chosindikizira, yonse ikhale monga maina ao, kwa mafuko khumi ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Miyalayo ikhalepo khumi ndi iwiri, uliwonse kuyimira dzina limodzi la ana a Israeli. Mwala uliwonse uzokotedwe ngati chidindo dzina limodzi la mafuko khumi ndi awiri a Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi miyalayi ikhale monga mwa maina a ana a Israyeli, khumindiawiri, monga maina ao; monga malocedwe a cosindikizira, yonse ikhale monga maina ao, kwa mafuko khumi ndi awiri.