Exodus 28:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Upange timaunyolo ta golide wabwino kwambiri ta pa chovala chapachifuwa, topota mwaluso ngati maukufu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Upangenso maunyolo pa chapachifuwa ngati zingwe, ntchito yopota, ya golide woona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Upange timaunyolo tagolide wabwino kwambiri ta pa chovala chapachifuwa, topota ngati chingwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Upangenso maunyolo pa capacifuwa ngati zingwe, nchito yopota, ya golidi woona.