Exodus 29:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono utenge nkhosa yamphongo inayo. Aroni ndi ana ake aamuna asanjike manja ao pamutu pa nkhosayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo utenge nkhosa yamphongo yinayo; ndi Aroni ndi ana ake amuna aike manja ao pamutu pa nkhosa yamphongoyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Utenge nkhosa yayimuna ina ndipo Aaroni ndi ana ake aamuna asanjike manja awo pamutu pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo utenge nkhosa yamphongo yinayo; ndi Aroni ndi ana ace amuna aike manja ao pamutu pa nkhosa yamphongoyo.