Exodus 29:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzadye zonse zimene adazipereka kwa Chauta pa mwambo wopepesera machimo poŵadzoza ndi kuŵapatula. Munthu wamba asadyeko, chifukwa nzoyera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adye zimene anachita nazo choteteza, kuti awadzaze manja ndi kuwapatulitsa; koma mlendo asadyeko, pakuti nzopatulika izi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adye zonse zimene anazipereka kwa Yehova pamwambo wopepesera machimo powadzoza ndi kuwapatula. Munthu wamba asadye chifukwa ndi zopatulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adye zimene anacita nazo coteteza, kuti awadzaze manja ndi kuwapatulitsa; koma mlendo asadyeko, pakuti nzopatulika izi.