Exodus 29:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pa guwa lansembe uziperekapo izi: nthaŵi zonse tsiku ndi tsiku, uzipereka anaankhosa aŵiri a chaka chimodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma izi ndizo uzikonza pa guwa la nsembelo; anaankhosa awiri a chaka chimodzi, tsiku ndi tsiku kosalekeza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsiku ndi tsiku pa guwa lansembe uzipereka izi: Ana ankhosa a chaka chimodzi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma izi ndizo uzikonza pa guwa la nsembelo; ana a nkhosa awiri a caka cimodzi, tsiku ndi tsiku kosalekeza.