Exodus 29:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwanawankhosa wina uzimpereka m'maŵa, wina madzulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwanawankhosa wina ukonze m'mawa; ndi mwanawankhosa wina ukonze madzulo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa muzipereka mwana wankhosa mmodzi ndipo winayo madzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwana wa nkhosa wina ukonze m'mawa; ndi mwana wa nkhosa wina ukonze madzulo;