Exodus 29:45 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakhala pakati pa anthu anga Aisraele, ndipo ndidzakhala Mulungu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzakhala pakati pa ana a Israele, ndi kukhala Mulungu wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakhala pakati pa Aisraeli ndikukhala Mulungu wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzakhala pakati pa ana a Israyeli, ndi kukhala Mulungu wao.