Exodus 29:46 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzandidziŵa Ine Chauta amene ndidaŵatulutsa ku Ejipito kuti ndikhale pakati pao. Ine ndine Chauta, Mulungu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova Mulungu wao, amene ndinawatulutsa m'dziko la Ejipito, kuti ndikhale pakati pao. Ine ndine Yehova Mulungu wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzadziwa kuti ine ndine Mulungu wawo amene ndinawatulutsa mʼdziko la Igupto kuti ndikhale pakati pawo. Ine ndine Yehova, Mulungu wawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova Mulungu wao, amene ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto, kuti ndikhale pakati pao. Ine ndine Yehova Mulungu wao.