Exodus 3:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono iwe ndikukutuma kwa Farao kuti ukatulutse anthu anga Aisraele ku Ejipito.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tiye tsopano, ndikutuma kwa Farao, kuti utulutse anthu anga, ana a Israele m'Ejipito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero tsopano, pita. Ine ndikukutuma kwa Farao kuti ukatulutse anthu anga, Aisraeli mʼdziko la Igupto.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tiye tsopano, ndikutuma kwa Farao, kuti uturutse anthu anga, ana a Israyeli m'Aigupto.