Exodus 3:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adamuyankha kuti, “Ine ndidzakhala nawe. Chitsimikizo chakuti ndakutuma ndine nachi: Utaŵatulutsa anthu anga ku Ejipito, mudzandipembedza pa phiri lomwe lino.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anati, Ine ndidzakhala ndi iwe; ndipo ichi ndi chizindikiro cha iwe, chakuti ndakutuma ndine; utatulutsa anthuwo m'Ejipito, mudzatumikira Mulungu paphiri pano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Mulungu anati, “Ine ndidzakhala nawe, ndipo ichi chidzakhala chizindikiro kwa iwe kuti ndine amene ndakutuma; Ukadzatulutsa anthu anga mʼdziko la Igupto, udzapembedza Mulungu pa phiri lino.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anati, Ine ndidzakhala ndi iwe; ndipo ici ndi cizindikilo ca iwe, cakuti ndakutuma ndine; utaturutsa anthuwo m'Aigupto mudzatumikira Mulungu paphiri pano.