Exodus 3:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adati, “Usayandikire pafupi. Vula nsapato zakozo, chifukwa malo waimapowo ngoyera.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anati, Usayandikire kuno; vula nsapato zako ku mapazi ako, pakuti pamalo pamene upondapo iwe, mpopatulika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu anati, “Usayandikire kuno. Vula nsapato zako, pakuti malo amene wayimapo ndi opatulika.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anati, Usayandikire kuno; bvula nsapato zako ku mapazi ako, pakuti pamalo pamene upondapo iwe, mpopatulika.