Exodus 30:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aliyense wolembedwa m'kalemberamo, wa zaka makumi aŵiri kapena kupitirira, adzapereke zimenezi kwa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yense wakupita kwa owerengedwawo, wa zaka makumi awiri ndi wa mphambu zake, apereke choperekacho kwa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense wolembedwa mu kawundula amene ali ndi zaka makumi awiri kapena kupitirira ayenera kupereka chopereka kwa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yense wakupita kwa owerengedwawo, wa zaka makumi awiri ndi wa mphambu zace, apereke coperekaco kwa Yehova.