Exodus 30:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati munthu wina apanga lubani wofanafana ndi ameneyu kuti amve fungo lake lokoma, azichotsedwa pakati pa anthu anzake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aliyense wokonza china chotere kununkhizapo, asadzidwe kwa anthu a mtundu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense amene adzapanga wofanana naye kuti asangalale ndi fungo lake ayenera kuchotsedwa pakati pa anthu anzake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ali yense wokonza cina cotere kununkhizapo, asadzidwe kwa anthu a mtundu wace.