Exodus 31:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
zovala zopatulika za wansembe Aroni ndi za ana ake, zomavala pa nthaŵi imene akutumikira,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi zovala zotumikira nazo, ndi zovala zopatulika za Aroni wansembe, ndi zovala za ana ake, zakuchita nazo ntchito ya nsembe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiponso zovala zonse zolukidwa, zovala zopatulika za Aaroni wansembe pamodzi ndi za ana ake, zovala pamene akutumikira monga ansembe,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi zobvala zotumikira nazo, ndi zobvala zopatulika za Aroni wansembe, ndi zobvala za ana ace, zakucita nazo nchito ya nsembe;