Exodus 31:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mafuta odzozera ndiponso lubani wa fungo lokoma, zonsezo zokhalira malo oyera. Adzapange zinthu zonsezi monga ndakulamulira iwe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mafuta odzoza, ndi chofukiza cha zonunkhira zokoma za malo opatulika; azichita monga mwa zonse ndakuuza iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiponso mafuta odzozera ndi lubani wonunkhira wa ku malo opatulika. Iwo azipanga monga momwe Ine ndinakulamulira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi mafuta odzoza, ndi cofukiza ca zonunkhira zokoma za malo opatulika; azicita monga mwa zonse ndakuuza iwe.