Exodus 31:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kulemba mapulani a ntchito zaluso ndi kugwira ntchito ndi golide, siliva ndi mkuŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kulingirira ntchito zaluso, kuchita ndi golide ndi siliva ndi mkuwa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kulemba ndondomeko ya ntchito zaluso ndi kupanga zinthu zagolide, zasiliva ndi zamkuwa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kulingirira nchito zaluso, kucita ndi golidi ndi siliva ndi mkuwa,