Exodus 31:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akudziŵanso kuzokota miyala yogwira nayo ntchito, kujoba mitengo, ndi kuchita zaluso zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuzokota miyala yoikika, ndi kozokota mtengo, kuchita ntchito zilizonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kusema ndi kuyika miyala yokongola, kukonza zinthu zamatabwa ndiponso kugwira ntchito ina iliyonse yamanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuzokota miyala yoikika, ndi kuzokota mtengo, kucita nchito ziri zonse.