Exodus 33:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anthu atamva mau oopsaŵa, adayamba kulira, ndipo panalibe ndi mmodzi yemwe amene adavala zovala zokongola.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anthu anamva mau awa oipa anachita chisoni; ndipo panalibe mmodzi anavala zokometsera zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu atamva mawu owopsawa, anayamba kulira ndipo palibe anavala zodzikometsera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anthu anamva mau awa oipa anacita cisoni; ndipo panalibe mmodzi anabvala zokometsera zace.