Exodus 35:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose adaitana Aisraele onse naŵauza kuti, “Chauta akukulamulani kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anasonkhanitsa khamu lonse la ana a Israele, nanena nao, Siwa mau amene Yehova anauza, kuti muwachite.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anasonkhanitsa gulu lonse la Aisraeli ndipo anawawuza kuti, “Zinthu zimene Yehova wakulamulirani kuti muzichite ndi izi:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose anasonkhanitsa khamu lonse la ana a Israyeli, nanena nao, Siwa mau amene Yehova anauza, kuti muwacite.