Exodus 35:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
choikaponyale ndi zipangizo zake, nyale zake ndi mafuta a nyalezo;
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi choikapo nyali cha kuunika, ndi zipangizo zake, ndi nyali zake, ndi mafuta a kuunika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
choyikapo nyale yowunikira pamodzi ndi zipangizo zake, nyale ndi mafuta anyalezo;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi coikapo nyali ca kuunika, ndi zipangizo zace, ndi nyali zace, ndi mafuta a kuunika;