Exodus 35:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
guwa lofukizirapo lubani ndi mphiko zake, mafuta odzozera, lubani wa fungo lonunkhira bwino, ndiponso nsalu zochingira za pa chipata cha chihema cha Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi guwa la nsembe lofukizapo, ndi mphiko zake, ndi mafuta odzoza, ndi chofukiza cha fungo lokoma, ndi nsalu yotsekera pakhomo, pa khomo la Kachisi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
guwa lofukizira lubani pamodzi ndi mitengo yake yonyamulira, mafuta odzozera ndi lubani onunkhira; nsalu yotchinga pa khomo lolowera mʼchihema;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi guwa la nsembe lofukizapo, ndi mphiko zace, ndi mafuta odzoza, ndi cofukiza ca pfungo lokoma, ndi nsaru yotsekera pakhomo, pa khomo la kacisi;