Exodus 35:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
nsalu zokoma kwambiri zovala anthu otumikira m'malo opatulika, ndiponso zovala zopatulika za wansembe Aroni ndi za ana ake, akamatumikira ngati ansembe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
zovala za kutumikira nazo m'malo opatulika, zovala zopatulika za Aroni wansembe, ndi zovala za ana ake, zakugwira nazo ntchito ya nsembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zovala zolukidwa zovala potumikira kumalo opatulika, zovala zopatulika za wansembe, Aaroni pamodzi ndi za ana ake aamuna pamene akutumikira monga ansembe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
zobvala za kutumikira nazo m'maopatulika, zobvala zopatulika za. Aroni wansembe, ndi zobvala za ana ace, zakugwira nazo nchito ya nsembe.